Ligi ya m'chigawo cha kumwera ya Thumbs Up iyamba pa 7 April mwezi wa mawa.

Mmodzi wa akuluakulu oyendesa ligi-yi, Raphel Humba watsimikiza izi poyankhula ndi Owinna.

28 Mar 06:32

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores