Timu ya Ntaja United yalengeza kuti yasaina katswiri womwetsa zigoli Goodson Shonga patsogolo pa ligi yachiwiri ya mdziko muno.
Shonga, yemwe wachokera kutimu ya Toreza Farm, wasaina mgwirizano wa zaka ziwiri kuti athandize timuyi kumwetsa zigoli.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores