Timu ya Civil Service United yasaina katswiri wosewera kutsogolo, Madalitso Maso, yemwe wasaina mgwirizano wa zaka zitatu.
Katswiriyu anali ku timu yaing'ono ya Civil komwe anachita ndipo atapatsidwa mpata mu mpikisano wa chigawo chapakati anakwanitsa kugoletsa zigoli ziwiri pa masewero atatu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores