Timu ya osewera mpira wa miyendo ya amayi ya dziko la South Africa - Banyana Banyana ikuyembekezeka kukumana ndi timu ya Malawi Scorchers pa masewero a paubale omwe achitike pa 5 ndi 8 April m'dziko la South Africa.
Izi zadziwika pomwe mphunzitsi wa timu ya dzikoli, Desiree Eliis amatulutsa ndandanda wa atsikana omwe atumikire mu masewero opimana mphamvuwa ndipo watenga osewera okwana makumi awiri ndi atatu (23).
Timu ya Banyana Banyana ikuyembekezeka kuzakhala ndi osewera awo onse omwe amadalira monga Linda MOTLHALO yemwe amasewera ku Scotland mu team ya Glasgow Rangers komanso Thembi KGATLANA.
Pepani munditumizile pa 0981658760
Tsopano munditumizile panambala iyi 0981658760
Mutumizileno pa 0981658760
Mutumizileno ku 0981658760
Tsopano mutumizile pa 0981658760
Kamba ka vuto la nambala yomwe tinapeleka kuti mutumizile ndalama za week yapa 10 to 16 Marc. Tsopano mutitumizile pa 0981658760. ZIKOMO.
TSOPANO MUTUMIZILE KU 0981658760
Takutumizirani ndalama zanuππ
Zikomo kwambili
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores