NKHANI
Masewero a pakati pa FCB Nyasa Big Bullets ndi Moyale Barracks mu chikho cha FDH ayamba 17:30hrs osati 5 koloko imanenedwa ija.
Izi zili chomwechi kamba koti bus ya Moyale inaonongeka pomwe anali kupita ku bwalo la Bingu zomwe zinachititsa kuti achedweko pang'ono.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores