Timu ya Mbeya City yaku Tanzania yatsimikiza kuti sinafikilidwe ndi timu ya Silver Strikers kuti agule katswiri wawo, Chimwemwe Idana, yemwe ali pangongole ndi timuyi.
Timuyi koma ipereka mwayi kwa Silver kuti akambirane za katswiri koma pokhapokha akafikilidwa.
Mgwirizano wa Idana wapangongole ku Silver ukuyembekezeka kutha kumapeto a mwezi uno.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores