Owinna yamvetsedwa kuti katswiri wina yemwe ankasewera Mighty Mukuru Wanderers mmbuyomo ndipo pano akusewerera timu Ina ya kunja ku maiko akummwera kwa Africa akhonza kubwereranso kutimuyi ngati sipakhala kusintha kulikonse.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores