Mphunzitsi watimu ya Silver Strikers wati timu yake, FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers ndi omwe alimbirane ukatswiri wa ligi ya TNM chaka chino ndipo palibenso ina.
Timu ya Silver Strikers ili ndi mapointsi 18 pamwamba pa ligi ndipo Bullets ndi Wanderers akubwera pambuyo pawo ndi mapointsi 17 aliyense.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores