Ndandanda wa matimu omwe atenge nawo mu mpikisano wa CAF wa chaka chino watuluka.
Pa ndandanda-wu timu ya kuno ku mudzi ya Bullets ilipo.