Karonga United yati ikhazikitsa timu ya mpira wa miyendo koma osewera ake atsikana ngati njira imodzi yofuna kukwanilitsa ndondomeko zomwe a CAF komanso a FAM anakhazikitsa.
Mlembi wa timuyi, Ramsey Simwaka wanena izi patsogolo pakuyamba kwa masewero a mpira wa miyendo chaka chino.
Malingana ndi a Simwaka iyi ndi njira imodzi yofuna kupititsa patsogolo masewero a mpira wa miyendo koma osewera ake atsikana.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores