Wosewera wa Flames Gerald Phiri wanyamuka mdziko la Sudan kupita ku Saudi Arabia komwe timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ikuchita zokonzekera zake.
Wosewera-yu akuyembekezeka kukhala pamodzi ndi timuyi patsogolo pa mpikisano wa Africa Cup of Nations (AFCON) omwe uchitikire ku Cameroon.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores