Osewera kutsogolo wa timu ya Nyasa Big Bullets, Babatunde Adepoju akutsogola ndi zigoli mu mpikisano wa Airtel Top 8.
Babatunde ali ndi zigoli ziwiri ndipo akutsatidwa ndi osewera wa Moyale, Lloyd Njaliwa, Martin Masoatheka wa MAFCO ndi Hassan Kajoke omwe agoletsa chigoli chimodzi aliyense.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores