Timu ya Mlatho Mponela yati itenga nawo mbali mu mpikisano wa Chipiku wa chaka chino.
Mmodzi wa akuluakulu a timuyi, Chiyamiko Litta, wati achita chotheka kuti abwelere mu ligi ya TNM.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores