Moni admin. Tithokoze kuti onse amene analosera bwino top 3 sabata yothera 21 June akuti alandira ndalama zawo. Koma amene analosera bwino top 3 sabata yothera 28 June akuti sanalandilebe. ZIKOMO.
Zikomo potsimikiza kuti omwe ameyenera kulandira sabata yatha alandira. Owina sabata yathanso alandira ndithu asakaike. Pepani kuti tachedwetsa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores