Pamene olosela a week ya mon 22 to sun 28 Jun. akuyembekezela kupeleka ma account awo. Tikufuna titsikimizile kuti olosela a week ya mon 15 to sun 21 Jun. sanalandilebe ndalama zawo m'paka lero . FUSO mungatifotokozele luti vuto ndichiyani?. ZIKOMO
Pepani kwambiri, tachedwetsadi kupereka ndalama ya sabata yothera 21 June. Tiyesetsa kutumiza za sabata yatha limodzi ndi za sabata yothera 28 June mkati mwa sabatayi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores