Moni admin wathu. Talandila dandaulo kuchokela kwa olosela bwino a week ya mon. 15 to sun. 21 June kuti sanalandibe m'paka lero ndalama zawo. Chonde aganizileni. ZIKOMO.
Pepani kwambiri, tipepese kuti tachedwetsa kupereka ndalama ya sabata yothera 21 June koma titumiza. Mutipepesereko kwa onse omwe awina.
Tiyesetsa kutumiza limodzi ndi za sabata yothera 28 June mkati mwa sabatayi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores