Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Malawi U23 national football team has won its first game from the three matches they have played in Belgium. The team won their first match today with 3 goals to 2 during their game against KRC Genk.
Malawi Under 23 National Football Team will play a training game against KRC Genk this afternoon in Belgium.
Malawi has already lost 2 training games in Belgium, in both matches conceding 3 goals.
Timu ya Malawi U23 yaluza ndi zigoli zitatu kwa chimodzi pa masewero ake achiwiri mdziko la Belgium.
Malawi U23 lero imasewera ndi OHL pa masewero opimana mphamvu.
Malawi Under 23 national football team will today play a training game in Belgium.
The Junior Flames will play against OHL.
Timu ya Malawi Under 23 lero ipitilira kuchita zokonzekera zake mdziko la Belgium.
Dzulo timuyi inaonera masewero amu mpikisano wa Europa a KRC GENK ndi Slavia Praag.
Bonanza yomwe timu ya Nyasa Big Bullets ichititse, padzakhala matimu anayi, awiri ochokera kunja kwa dziko lino, ndipo kuno ku Malawi izakhala Noma ndi Bullets.
Mkulu woyendetsa ntchito za Nyasa Big Bullets, Fleetwood Haiya, wati zokonzekera zonse za bonanza yomwe akonza kumayambiliro a mwezi wa March zili mchimake.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Malawi Under 23 lero masana isewera masewero ake oyamba mdziko la Belgium ndi STVV. Timu ya dziko lino-yi inachita zokonzekera zake kukonzekera za masewero-wa.