Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
HARRY NYIRENDA WATSANZIKA KU HAMMERS
Mtsogoleri wa timu ya Ekwendeni Hammers, Harry Nyirenda, watsanzika kutimu yakeyi pomwe tsopano wachoka kutimuyi kukayang'ana mwayi ku matimu ena.
Imodzi mwa tsamba lolemba nkhani mdziko muno, Wa Ganyu, yatsimikiza za nkhaniyi ponena kuti Nyirenda watsanzika pomwe zamveka kuti apita ku timu Ina.
Iwo ati timu ya Civo United yatsegula zokambirana ndi katswiriyu ndipo amapatsa zomwe angakwanitse kumupatsa katswiriyu ndipo alingalira pomwe matimu enanso awiri akumufuna.
Nyirenda anapita ku timuyi mu chaka cha 2019 pomwe anachotsedwa ku timu ya Mighty Mukuru Wanderers yomwe anapitako mu 2016 atachoka ku Black Leopards yaku South Africa.
Former BE FORWARD Wanderers defender, Harry Nyirenda, has joined Ekwendeni Hammers, the club has announced.
Lucky Malata, Harry Nyirenda, Peter Katsonga and Zicco Mkanda have been fired at BE FORWARD Wanderers.
The team has confirmed the development through a statement they issued on Friday.
Wanderers yatsutsa malipoti oti yasiya osewera ena monga mmene anthu akunenera pa masamba a mchezo a intaneti.
Anthu ena akufalitsa kuti timuyi yasiya Alfred Manyozo komanso Harry Nyirenda kumpoto.
Timu ya BE FORWARD Wanderers ikuyembekezeka kuchotsa osewera ena ku timu-yi season ya 2019 isanayambe.
Peter Wadabwa ndi Harry Nyirenda ndi ena mwa osewera omwe atha kuchotsedwa.
-- Malawi Line Up -- Charles Swini Stanely Sanudi John Lanjesi Francis Mulimbika Harry Nyirenda Josephy Kamwendo Peter Wadabwa Wonderful Jereman John Banda Rafique Namwela Chiukepo Msowoya