gayz tatiuzeni zoona zikutha bwanji,noma ndi hongover
kodi BFW agula osewela angati atsopano ndipo ndi ndani ndi ndani
Yasaina China Chirwa ndi Eric Atsiga
BFW kuti moti buuuuuuu
BFW tikufunika kuti gemu yathu yoyamba ndi KB tikufunika kuzawina osazapanga zomwe munapanga ndi moyare zimenezo ndiye zopusa tidanyozeka kwambiri .