Katswiri watimu ya FCB Nyasa Big Bullets, Chikumbutso Salima, wasankhidwa kuti wasewera bwino mu mwezi wa December kutimuyi.
Iye wagonjetsa Babatunde Adepoju, Khumbo Banda ndi Wongani Lungu kuti atenge mphotoyi.
Salima wakhala osewera ofunikira ku timuyi mu ligi ya 2025 pomwe anamwetsa zigoli 15 ndi kuthandiziranso zina 11.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores