Timu ya Dedza Dynamos yatsimikiza kuti otseka kumbuyo wawo, Godfrey Kanyika, wachoka kutimuyi pomwe walowera kutimu ya Ekhaya FC.
Timuyi yamufunira zabwino zonse pomwe akusiya thumba la Meja kupita ku butchale.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores