Timu ya Blue Eagles yalengeza kuti yatenga goloboyi Elias Missi kukhala m'modzi mwa iwo kutsatira Kuchoka kutimu ya Ekhaya.
Missi anali mu gulu la magoloboyi omwe achinyitsa zigoli zochepa mu ligi Koma anali pa chilango kamba komufinya khosi Babatunde Adepoju.
Iye walowa mmalo mwa Joshua Waka yemwe anapita ku Ekhaya.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores