NKHANI
Timu ya Silver Strikers ikufuna katswiri wa Mighty Mukuru Wanderers, Vitumbiko Kumwenda, kuti apite kutimu yawo pangongole ya miyezi isanu.
Timuyi yalembera Wanderers pa nkhaniyi ndipo yati palibe nkhani pa zokudza malipiro ake poti iyang'anira zonse pa nkhaniyi.
Osewera angapo a Wanderers monga Vincent Nyangulu, Francis Mkonda komanso ena akuyembekezeka kupita pa ngongole ku matimu ena pomwe nthawi yawo yosewera yachepa kutimuyi.
Source: Wa Mpira
ππΏπ
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores