Timu ya Silver Strikers yapereka mphoto kwa osewera komanso adindo ena omwe anachita bwino chaka chatha kutimuyi.
Mabankers anachititsa mwambo opereka mphoto-zi ku ofesi zawo mu mzinda wa Lilongwe.
Iyi ati ndi njira imodzi yolimbikitsa osewera komanso adindo kutimuyi kulimbikira ntchito.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores