Bungwe la Football Association of Malawi mogwirizana ndi bank ya NBS apereka makaka omwe matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Silver Strikers agwiritse ntchito pa masewero amu Charity Shield lowerukali.
Bungweli lachita izi lachinayi pa mwambo wa mdipiti omwe umayenda mu mzinda wa Lilongwe pofalitsa za bankiyi ndi mpikisanowu.
Matimuwa akumana Loweruka pa bwalo la Bingu ndipo ndalama zomwe zipezeke zidzagwira ntchito yogulira zipangizo zolimbikitsa za ukhondo my sukulu za ku Lilongwe.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores