Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
General Secretary - Samuel Mponda, Vice General Secretary - Charles Andrew, Treasure - Rahim Latif, Vice Treasure - Kennedy Kemosi.
Timu ya Wanderers ikugwilitsa ntchito njira yoti anthu aziima kumbuyo kwa munthu woyimira ndi kuyamba kuwerenga anthu.
Anthu ena njirayi sakugwiliza nayo.
Anthu-wa ati oimira ena apeza mapanza.
Samuel Mponda returns his seat in new Wanderers Supporter Committee despite his contestant disputing the results.
He is the new General Secretary of the committee.
Civil Service United will start 2020 football preparations next week.
Team Manager for the club, Gabriel Chirwa, has confirmed the development.
Chirwa says they will bring in new players.
Lero Wanderers ikuchititsa chisankho chosankha komiti yatsopano ya masapota.
Chisankho-chi chikuchitikira mu mzinda wa Blantyre.
Members; Anton Chawanda, Dalitso Robert, Cecilia Kananji, Peter Mvalo and Austin Saini.
Wanderers Supporters Chairman - Melvin Nkunika
First Chairman - Witness Kanyemba
Second Chairman - Dines Chitsulo
Gabadinho Mhango continues to shine in South Africa as he is topping the Absa Premier League.
On Saturday Mhango scored a brace to help Orlando Pirates beat Chipa United 2-1.
Mhango has now scored 14 goals in 18 games.
Osewera akale a timu ya Nyasa Big Bullets lero asewera ndi SR Socials pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Wosewera wa Kamuzu Barracks, Francisco Kamdzeka, wakhala katswiri omwetsa zigoli zochuluka mu mpikisano wa 2019 FISD Challenge Cup. Kamdzeka anagoletsa zigoli 5 mu masewero omwe timu yake inali nawo.
FISD Limited Company hints on increasing their sponsorship next year.
Company's Executive Director, Frank Mwenechanya, said this during 2019 FISD Challenge Cup presentation in Lilongwe on Friday.
Zambian tactician, Daniel Kabwe, has arrived in the country ahead of his big task of lifting all trophies with Silver Strikers.
Kabwe has been appointed as Silver Strikers new coach.
Silver Strikers says 17 players that have been chopped by the club recommendations were made by previous technical panel.
Bungwe la FAM lalingiza wosewera kuti atsatire malamulo onse pa nthawi yomwe akusintha timu.
Mmodzi wa akuluakulu ku FAM, Casper Jangale, ndiye wapereka malangizo-wa.
Walter Nyamilandu lero ndi tsiku lomaliza kugwira ntchito ku kampani ya Illovo pomwe wati akufuna kulunjika chidwi chake potukula masewero a mpira.
Izi zatsimikizidwa m'chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa chomwe chatsimikiza za kusiya ntchito kwa a Nyamilandu.
Kampani ya FISD pamodzi ndi bungwe la FAM mawa apereka mphoto kwa matimu komanso wosewera amene anachita bwino mu chaka cha 2019.
Mkulu oona zamipikisano ku FAM, Gomegzani Zakazaka, watsimikiza za izi.
Chitipa White Movers has started 2020 football preparations ahead of SIMSO kickoff.
Team Manager for the club, Stephen Sibale, has confirmed this through a press statement.
Silver Striker says they will allow their new head coach, Daniel Kabwe, to buy players from other countries.
Chairperson for the club, Victor Madhlopa, said this in an interview.
Timu ya Wanderers yati mu 2020 ikufuna iyambe kuyendetsedwa ngati kampani ndi cholinga choti ayambe kupanga mphindu lochuluka kumpira.
Oyang'anira wosewera ku timuyi, Victor Maunde, ndiye wanena izi
Former Silver Strikers player, Chawanangwa Kaonga, is yet to be cleared to start playing for TS Sporting in South Africa.
Reports indicate that before joining the club, Kaonga had a running contract.
kondi Ekwenden hummers yasankha stadium iti?
Zambian League ranked 55th in the world and 5th in Africa.
Below are 100 Strongest League in the world.
Players have been advised to avoid social football during the off season.
FAM Club Licensing and Compliance Manager, Casper Jangale, said this in an interview with Owinna.
Akuluakulu a Wanderers awapempha kuti akhazikitse komiti yapadera yoyendetsa chisankho.
Mmodzi wa masapota wa Wanderers, Slyvester Luka, ndiye wapereka pempholi.
MBC Stand Supporters Initiative has announced the change of its name to Mpira Umodzi Supporters Initiative.
The executive committee of the grouping agreed this at a meeting which was held in Blantyre
Wosewera wakale wa Flames komanso Wanderers wati masewero ake omaliza, Ceremonial game m'chingerezi akhalapo pa 7 February.
Kamwendo watsimikiza izi poyankhula ndi Owinna.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Flames lero iyamba zokonzekera za m'zigawo.
Zokonzekerazi zikhalapo m'zigawo za Mzuzu, Lilongwe komanso Blantyre.
Wosewera 30 a mdziko muno ndiwo atenge nawo mbali pa zokonzekerazi.
Flames player, Chikoti Chirwa, has signed a 1 year contract with Amazulu.
Agent of the player, Prince Jere, has confirmed the development.
According to Jere, Chikoti will be loaned to Royal Eagles.
Football Association of Malawi (FAM) has launched CAF D Coaching License in the country.
FAM Technical Director, John Kaputa, has confirmed this to Owinna.
Football Association of Malawi (FAM) has announced that e-ticketing will first be used during this year's FAM Charity Shield.
FAM will announce in due course venue of the games.
Robin Ngalande has terminated his contract with Zire FK in Azerbaijan.
Ngalande says reasons of the termination are best interest of him and the club.
Leo Mpulula, wasankhidwa kukhala mphunzitsi wa Silver Strikers Reserves.
Mpulula anali mmodzi wa aphunzitsi yemwe anafunsira ntchito ku timu yaikulu ya Silver.
Silver Strikers have employed Zambian tactician, Dan Kabwe, as new head coach.
Kabwe who applied for the post was successful after beating other 12 coaches.
Kabwe has replaced, Young Chimodzi.
Bungwe la COSAFA latsimikiza kuti dziko lino lichititse mpikisano wa wosewera mpira wa miyendo koma osapyola za 17 chaka chino.
Izi zatsimikizidwa pa mkumano omwe mamembala a bungweli anali nawo.
FAM has reached a consensus with Sulom and Super League teams to implement e ticketing in 2020 football season to maximize gate revenue.