Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Uganda vs Malawi
Coach wa Flames wakhulupilira Anyamata omwe anayamba ndi South Sudan lachitatu lathali,lero pa Nelson Mandela Stadium ku Uganda.
Koyenera kuti ayambe Anyamata omwe aja kapena akuyenera kusintha?
Asinthe
Mtopwa mawaso iwina
Zambia vs I Cory coast
Mpikisano ofuna kukhala otsogolera bungwe la FAM ukhalapo pakati pa Mwenda ndi Nyamilandu kutsatira kusankhidwa ndi nthumwi za bungwe-li kuti akaime pa chisankho-chi.
Flames have safely arrived in Kampala, Uganda ahead of Sunday's encounter against the Cranes.
The team is lodging at Hotel Africana and they are expected to have their first training this afternoon.
Despite signing a 3 year contract with Silver Strikers this season, Mphatso Dzongololo, will play for the Lilongwe giants next season.
Confirmed reports indicate that the player is yet to be cleared.
Central Region Football Association (CRFA) has postponed all Division one games slated for tomorrow, Saturday.
This follows the death of Make Sure Pirates Player, Blessings Mhango.
All is set for Schumacher Kuwali to join Mozambique based club, UD Songo at the end of the season.
Blue Eagles Chairperson, Alexander Ngwala, confirmed the development to Owinna.
*Khuda Muyaba misses the Uganda Trip*
The current TNM Super League Top Goal Scorer, Khuda Muyaba, has not travelled to Uganda ahead of Flames game on Sunday with the country's national football team.
*SAD NEWS*
Former Flames Player, Elvis Kafoteka, has lost his Wife who was involved in an accident along Lilongwe By Pass Road.
The deceased Thoko was working with Ntcheu Traffic Police.
Akatswiri okonda masewero mdziko muno ati ndandanda wa osewera omwe waitanidwa ku U-20 ambiri mwa iwo ndi oposa zaka 20.
Humphrey Mvula, wanena izi patsogolo pa zokonzekera za timuyi lero.
Flames is topping 2021 Afcon qualifiers group B with 3 points following a win over South Sudan.
Gabadnho Mhango scored the lone goal for the Flames after beating 4 defender's in the 6 yard box.
Zambia
Malawi National Football Team commonly known as the Flames have won their first match in 2021 Afcon competition after beating South Sudan 1 nil.
Mhango scored the lone goal for the Flames at 68.
Tiwina Lero Malawi 1:0 South Sudan
Mukanalosera mpira usanayambe, tikanawerengera kuti munalosera molondola.
Fam President Walter NYAMILANDU visited the boys yesterday and told them to start the campaign on high note with a big win and not underrate South Sudan
Kulephera kwa FAM kupereka zinthu zoyenera kwa otsatira a timuyi ati ndiko kumapangitsa anthu ochepa kubwera ku masewero a Flames.
Mmodzi wa akuluakulu wa masapota a Flames, Billy One, wanena izi.
Malawi Under 20 National Football team Coach Peter Mponda has named a 34-man provisional squad.
This is according to a statement released by FAM Competition Manager, Gomegzani Zakazaka.
Akuluakulu a Bullets ati adikira lipoti la aphunzitsi pomwe akhale akuchotsa osewera ena ku timuyi.
Mmodzi wa akuluakulu a Bullets, Albert Chigoga, ndiye wanena izi.
Timu ya Red Lions yibwelera mu ligi ya TNM kutsatira kuchita bwino mu ligi ya kumwera ya ThumbsUp.
Izi zili chomwechi kaamba koti timuyi yafika pa mlingo wa mapoint omwe matimu ena safika.
Osewera atatu a flames omwe afika dzulo,apanga nawo zokonzekera ndi anzawo chigawo cha mamawa.
Gabadinho, Papa komanso Mbulu.
Captain John CJ Banda wafika usiku wathawu
Flames Coach, Meke Mwase, is upbeat for a win in Wednesday's encounter against South Sudan.
Speaking to Owinna, Mwase said his charges are geared up for the game.
Football Association of Malawi (FAM) says FISD semifinals will be played on 23 and 24 November.
FAM Competitions Manager, Gomegzani Zakazaka confirmed the development.
Gerald Phiri, Gabadinho Mhango and Richard Mbulu have arrived in the country today.
The three are in ahead of their Afcon game against South Sudan on Wednesday at Kamuzu Stadium.
Top goal scorer
Khuda Muyaba is leading with 15 goals followed by Babatunde and Kajoke.
Kulephera kumwetsa zigoli zochuluka ku timu ya Bullets ati ndi vuto lomwe likupangitsa timuyi kusachita bwino m'masewero ake ochuluka.
Pasuwa wanena izi kutsatira kutuluka kwa timuyi mu FISD.
Osewera wa Blue Eagles, Schumacher Kuwali, wauza Bullets kuti ikonzekere kuzathamanga komanso kuzagonja pa masewero omwe akhale nawo mu ligi ndi timuyi.
Matimu a Bullets komanso Wanderers ati achirimika pofuna kutenga ukatswiri wa ligi ya TNM kutsatira kutuluka kwawo mu mpikisano wa FISD.
Akuluakulu a matimu awiri-wa auza izi Owinna.
Ok