Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Five BE FORWARD Wanderers players have extended their stay at the club.
The five are; Alfred Manyozo, Lucky Malata, Stanley Sanudi, Isaac Kaliati and Richard Chipuwa.
Lucky Malata wabwelera ku timu ya BE FORWARD Wanderers.
Mlembi wa timuyi, Victor Maunde, watsimikiza za izi.
Malingana ndi Maunde, wosewera-yu wapepesa ku timuyi.
Owinna yapeza kuti timu ya Silver Strikers ilibe chidwi chosaina wosewera wakale wa timuyi, Lucky Malata.
Malingana ndi anthu omwe Owinna yayankhula nawo ku Silver Strikers aphunzitsi a timuyi sanayankhulepo zofuna wosewera-yu.
Lucky Malata, Harry Nyirenda, Peter Katsonga and Zicco Mkanda have been fired at BE FORWARD Wanderers.
The team has confirmed the development through a statement they issued on Friday.
Flames have safely arrived in the country from Uganda after suffering a 2 nil defeat against Cranes.
Lucky Malata, Gabadinho Mhango, Gerald Phiri Jnr and Richard Mbulu are expected to arrive today.
Wanderers starting XI: W. Thole; D. Chembezi, L. Malata, E. Astigah, T. Sumani, A. Manyozo, F. Zulu, F. Madinga I. Kaliati, B. Adepoju, V. Nyangulu.
Flames Head Coach, Meke Mwase says he is impressed with how Khuda Muyaba and Lucky Malata have performed at training for a week.
Mwase remarks follows the duo absent for some time in Flames Camp.
Atalengeza kuti sadzatumikiraso timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino, Lucky Malata, waitanidwa kuti atenge nawo mbali pa zokonzekera za Flames kuyambira Lolemba.
Osewera kumbuyo kwa Wanderers, Lucky Malata ndi Francis Mulimbika, anayendera osewera wa Bullets, John Lanjesi, yemwe ndi ovulala.
Osewera onse-wa amasewera kumbuyo.
Lucky Malata and Peter Cholopi have resumed to training with Wanderers this week.
The duo were in South Africa on trials at Free State Stars.
FT: Silver Strikers 4 - 0 EPAC (2x Peter Wadabwa, Lucky Malata, Green Harawa)
FT: Silver Strikers 2 - 3 Blue Eagles (Peter Wadabwa, Green Harawa - Micium Mhone, Elia Kabingu, Lucky Malata (O.G))
FT: Karonga United 0 - 2 Silver Strikers (Lucky Malata, Blessings Tembo)