Kampani ya Universal Industries yapereka madzi akumwa ku timu ya Bullets ngati njira imodzi yowalimbikitsa masewero awo amu CAF Loweluka likudza-li.