Timu ya Mighty Wanderers yati yaphunzira zambiri kuchokera kwa anzawo a Nyasa Big Bullets chaka chino.
Malingana ndi Wanderers, chachikulu chomwe aphunzira ku Bullets ndikulimbira pa masewero komanso kusintha kachitidwe ka zinthu zawo.
Timuyi yati ichirimika chaka cha mawa mu mpikisano yomwe atenge mbali.
chakachino muyesense mutenge chikho chimonzi chokha
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores