Mtsogoleri wa bungwe la FAM Walter Nyamilandu wati akufuna kukhazikitsa ndondomeko zoti aphunzitsi amasewero osiyanasiyana azigwilitsa ntchito njira zamakono monga makina a computer.
A Nyamilandu ati izi zithandizira kuti ntchito yawo izikhala yosavuta.
Iwo ati maiko ambiri pakadali pano akugwilitsa njirazi poona momwe matimu anzawo akuchitira komanso kusunga uthenga ofunikira.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores