Mtsogoleri wa bungwe la Football Association of Malawi (FAM) Walter Nyamilandu wati aonetsetsa kuti timu ya Flames ikupitilira kuchita bwino m'mipikisano yomwe ikutenga mbali.
A Nyamilandu anena izi pambuyo polandira bus yatsopano kuchokera ku banki ya FDH yomwe Flames izigwilitsa ntchito.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores