Timu ya Nyasa Big Bullets isewera masewero 3 m'masiku 8 kuyambira mawa Lachitatu.
Masewero-wa ndi amu ligi ya TNM.
Mawa, Bullets isewera ndi Red Lions pamene Sunday isewere ndi Civil Service United asanakumane ndi Sable Farming Lachitatu sabata yamawa.
Bullets ili pa namba 1 mu ligi-yi ndimapoint 52 pa masewero 20 omwe yasewera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores