Wosewera wa Flames Robin Ngalande wasaina mgwirizano ndi timu ya Mighty Mukuru Wanderers.
Izi zadza pamene mgwirizano wake ndi timu ya dziko la Ethiopia ya St George watha.
Ngalande watsimikiza za nkhaniyi pamene wati matimu ochuluka amafuna koma wasankha kutumikira manoma.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores