Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Flames isewera masewero ake apakhomo a Ivory Coast mdziko la South Africa.
Awa ndi masewero a mpikisano a World Cup Qualifiers.
Izi zikutsatira kukana kwa bungwe la CAF kuti timuyi igwilitse ntchito bwalo la Bingu lomwe amalikonza.
Malingana ndi nthumwi za CAF bwaloli sili kufikira zonse zoyenera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores