Timu ya Mighty Wanderers yayamikira Dr. Thomson Mpinganjira kaamba kowathandiza ndi ndalama.
A Mpinganjira apereka ndalama zokwana 20.2 million Kwacha zoti timuyi ipereke malipiro.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores