Timu ya Chitipa United yasankha, Christopher Nyambose, kukhala mphunzitsi wogwilizira wa timuyi.
Mlembi wa timu ya Chitipa United, Duma Ngoma, watsimikiza za nkhaniyi.
A Nyambose akulowa m'malo mwa Alex Ngwira omwe asiya kuphunzitsa timuyi mwezi wa January
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores