Mtsogoleri wa bungwe loyendetsa masewero a mpira wa miyendo mdziko muno la FAM, Walter Nyamilandu, walimbikitsa anthu okhudzidwa ndi masewerowa kutsatira njira zopewera matenda a COVID-19.
Mtsogoleri wa FAMyu wati kuimitsidwa kwa masewero kwa sabata zitatu kusabwenze anthuwa mbuyo potsatira ndondomekozi.
Iwo ati posachedwapa anthu akhala akuonera masewero a mpira.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores