Mkulu wa timu ya Ntopwa, Isaac Jomo Osman, wati kumangidwa kwake ndi kaamba ka anthu ena ake omwe ali ndi mphamvu zochuluka.
Osman wati akumangidwa pa zinthu zomwe zinachitika kalekale.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores