Nzika za dziko lino zomwe zinachoka ku South Africa zokwanira 400 zathawa pamene amazisunga pa bwalo la Kamuzu.
Nzika-zi zathawa pamene zimadikira zotsatira zawo molingana ndi matenda a Covid-19.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores