Katswiri wa nkhani za masewero, Kelvin Moyo, wati bungwe la FAM litambasule bwino lomwe momwe mipikisano ya zaka zikubwera iziyendera mdziko muno.
Izi zikudza pomwe FAM yati mipikisano ya chaka chino iyamba mu August.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores