Owinna yapeza kuti timu ya Silver Strikers ilibe chidwi chosaina wosewera wakale wa timuyi, Lucky Malata.
Malingana ndi anthu omwe Owinna yayankhula nawo ku Silver Strikers aphunzitsi a timuyi sanayankhulepo zofuna wosewera-yu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores