Timu ya Blue Eagles iyamba zokonzekera za mipikisano ya 2020 lero masana.
Ofalitsa nkhani wa timuyi, Steven Kumalonje, watsimikiza za nkhaniyi.
Zokonzekera-zi ati azipangira mu mzinda wa Lilongwe.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores