Khuda Muyaba wati iye ndi osewera wa pa mwamba kuposa anzake onse mu chaka cha 2019.
Muyaba wanena izi kutsatira mphoto zosiyanasiyana zomwe wapeza mu chaka-chi.
Mu chaka cha 2019 Khuda Muyaba wakhala katswiri omwetsa zigoli zochuluka mipikisano ya Airtel Top 8 ndi TNM Super League.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores