Nthumwi zomwe zimavota kuchokera kumpoto ati zalandira kalata lero kuti akakhale nawo pa mwambo okhazikitsa mfundo wa a Nyamilandu.
Mlembi wa bungwe la NRFA, Masiya Nyasulu, wauza izi Owinna.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores