Owinna yapeza kuti mabwalo a zamasewero, omwe boma likufuna kumangira Bullets ndi Wanderers, adzakhala m'manja mwa Sports Council ngati aphungu awavomeleze. Izi ndi zomwe ena pa pulojekiti-yi atiuza.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores